spot_img
27.2 C
New York
Thursday, June 13, 2024
spot_img

FCB Nyasa Big Bullets waku CAF

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yatsimikiza zosewera nawo mu mpikisano wa Confederation for African Football (CAF) chaka chino kupatula kuti yakhala isakuchita bwino zaka zapitazi.

M’modzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito za timuyi Albert Chigoga wati pakali pano akuluakulu akukambirana zoti timuyi isewere mu CAF Champions kapena CAF confederations penena kuti ali ndi zodziyenereza kusewera mipikisano yonseyi.

Katswiri pa zamasewero mdziko muno Charles Nyirenda walangiza akuluakulu atimu ya Bullets kuti akonzekere bwino mpikisanowu kuti akachite bwino.-CAPITAL FM

Related Articles

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisement -

Latest Articles