spot_img
21.4 C
New York
Thursday, May 23, 2024
spot_img

Sugar wakwera mtengo

Kampani yopanga Sugar ya Illovo Malawi Plc yalengeza za kukwera kwa mitengo ya Sugar kuyambila lero.

Kalata yomwe kampaniyi yatulutsa yatsimikiza za kukwera kwa mtengoku.

Mwazina, kalatayi yati brown Sugar olemera 1 kilogalamu adzigulitsidwa pa mtengo wa 2,300 kwacha pomwe sugar woyera olemera 1 kilogalamu adzigulitsidwa pa mtengo wa 2,600 kwacha.

Kukwera mtengoku kwadza ngakhale aMalawi ambiri akulephera kupeza sugar pa msika, zomwe zapangitsa kut ogulitsa malonda nawo akweze mtengo kufika pa K3 500 pa pakeyi yomweyi.

Related Articles

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisement -

Latest Articles