Malawi President Rev Dr. Lazarus Chakwera on Friday appointed a special cabinet committee public private partnership comprising of four Malawi Congress Party (MCP) members and one each for UTM and Peoples Party.
According to a press statement signed by Chief Secretary to the Government Zangazanga Chikhosi, the committee will be chaired by country’s Vice President Dr. Saulos Chilima.
Other committee members are Minister of Finance Felix Mlusu, Minister of Transport and Public Works Sidik Mia, Minister of Labour Ken Kandodo, Minister of Energy Newton Kambala, Minister of Trade Sosten Gwengwe and Minister of Industry Roy Kachale Banda.
The statement said the PPP Cabinet committee will act as an effective platform for the regular consultations between the private and public sectors.
The committee will also ensure that business environment is competitive and supports the development of public private partnerships as well as the creation and attraction of new businesses.
Zitayeni izi zingokupatsanipo chabe BP. The same Chilima you castigated is the one chairing this committee. DPP will never come back to power and the rumour is that Atupele wants to dump DPP for Tonse alliance. The level of theft and impunity propagated by the DPP administration has shocked him to the core.
Who castigated chilima? This guy is power hungry no wonder he is working as the president. There is no way a ship can have two captains. Ikakhala nkhani yambava, mbava zenizeni ndiizi. Akumanga dala a dpp ncholinga choti akasololasolola akadzakwizingidwa azidzati nanga apm yo bwanji popeza anaba cement….zaziiii. Cabinet ndi cabinet, makomiti ndi makomiti, chilichonse chilima koma ayi mia akhaleponso, alipo okha mmalawi muno?. Mukaonetsetsa apa chakwera palibe chomwe akupanga and akuyendetsa boma ndi chilima ndi mia. Chomwe amadziwa chakwera ndikunyengerera anthu kuti amuthandize atsogole kuti adzawapatse maudindo ndi mwayi wamabisinesi koma luso loyendetsa zinthu alibe. And our democracy is at risk of ending. Amakhothi ndiawo akuonetsa kufinya anthu and popanda mkumano wachilima ndi akazembe aja chisale sakanatuluka pa bail. Apapa atupele akangozigulitsa ku mcp zionetseratu dyera komanso kusakhwima pandale kwa atsogoleri athu andale. Chipani chokhacho chomwe mission yake ndi kuthandiza anthu osati kugula anthu kuti chiziba ndi chadpp under apm and bingu. Iwo sali monyengerera anthu koma ntchito igwirike. Mundivomereza awa akhalira ma press conference pomwe amnzawo zinkangogwira ntchito mpaka hrdc kumaleresa kuti ayi ayi adpp mwaonjeza kwinako siilani amnzanu azapangeko nawo kachitukuko. Amipingo dpp amadana nayo chifukwa ikafuna kumanga zipatala, masukulu, makoleji, etc simacheza and iwo ma private awo monga zipatala, masukulu, etc, zimakhala pachiopsezo. Tangoganizani ndi wa private uti angalole kuti mmalawi muno mudzimangidwa masekondale 250 iye angokhala duuu. Even jb zimampweteka chifukwa ndiye kuti kafoundation kake kaja basi, kuyambira aphunzitsi, makhukhi, azilonda, ana asukulu, etc, onse akhala nyomiiiii kubalalikira kuboma. Mumuuze mtambo kuti mapresser ake ife tatopa nawo, koma akhale muofesi agwire ntchito tione apanga chani? Palibe uyo akumusokoneza ndi ma violence and thats the way dpp operates: Kuoposition angakhale m’boma iwo ndi madolo pakayendetsedwe kadziko osamangokhalira kuganiza zamastate visits, mpaka maiko khumi kumyendo ati okapemphetsa. Amnzanu amagaya zingini zamommuno mpaka boma laUS mkugoma limvekere koma na prof delivery alibe mnzake tiyeni timpatsenso kagawo kena kamileniyamu chalenji kopoleshoni. Iiiii koma zinazi inu bola kungozicheka.