spot_img
spot_img
6.6 C
New York
Thursday, November 14, 2024
spot_img
spot_img

Boma ndi lomweli, Chakwera apitiriza kulamulira,Yatero MCP

Yemwe anali phungu wa dera lapakati ku Zomba, Mai Patricia Kainga Nangozo, wati wina afune asafune, mtsogoleri wa dziko lino, a Lazarus Chakwera, apitiriza kulamulira dziko lino.

A Kainga Nangozo ayankhula izi pa bwalo la St. Martin’s ku Zomba Thondwe komwe, wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha MCP, a Catherine Gotani-Hara akuchititsa msonkhano wa ndale.

Iwo ati izi zikhala chonchi chifukwa choti a Chakwera anaika maziko a mphamvu pokweza ndalama ya chitukuko cha ku dera la Constituency Development Fund (CDF).

Dziko la Malawi ikuyembekezereka kuzakhala ndi chinsankho chosakha mtsogoleri wa dziko, aphungu komanso makhasala chaka cha mawa.

Related Articles

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisement -

Latest Articles