spot_img
Saturday, December 14, 2024
spot_img
HomeBusinessMowa wa Castel wakwera mtengo

Mowa wa Castel wakwera mtengo

Mitengo ya katundu ofunukira kwambiri pa moyo wa munthu monga “mowa” ikupitilira kukwera mitengo mdziko muno.

Pakadali pano, Kampani yofulula mowa ya Castel Malawi yalengeza za kukwera mtengo kwa wina mwa mowa wake kuyambira lero.

Mowa omwe wakwera ndi Carlsberg Chill kuchoka pa K1,500 kufika pa K1,600 botolo ndipo Carlsberg Green ndi Special Brew wa botolo la 330ml wika pa K1,500 kuchoka pa K1,400.

Carlsberg Green ndi Special wamkulu (Petroda/Winto) komanso mowa wina monga Kuchekuche, Castel, Doppel Munich ndi Pombe Breeze zinakali pa mitengo yakale yomwe ija.

RELATED ARTICLES

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisment -

Most Popular