spot_img
Saturday, December 14, 2024
spot_img
HomeLatestA Chilima kulibe

A Chilima kulibe

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Dr. Saulos Chilima amwalira.

Mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera walengeza izi ponena kuti anthu onse khumi amene anali mu ndege yomwe inanyamula a Chilima dzulo kupita nawo ku Mzuzu amwalira.

“Ndikudziwa kuti kwa aliyese kwa ife tikunva kupweteka komanso kukhala kakasi pa nthawi yotere ndipo nyengo imeneyi imatipangitsa kukwiya chifukwa timakhala ndimafunso ambiri. Ndikumvetsa chifukwa nanenso ndikumva chimodzimodzi.

“Pemphero langa ndiloti Mulungu atitonthoze tonse ndikuchiza mabala okudza ndi ngozi imeneyi.”

RELATED ARTICLES

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

- Advertisment -

Most Popular