What Is Chakwera Bringing Us? Za Kamuzu?

Kamuzu
Dr Laz at zii, akukonza mavuto awo mu MCP. Kaya zitheka, sizikudziwika. They have had divisions but now they are having divisions on the divisions.

Anyway, there are some people that seriously believe that antha kukonza zinthu ndikukhalanso ndi nthawi ya campaign ndikuwina masankho yangotsala miyezi yochepayi kuti chichitike.

Funso ndilaku, panthawi iyi Dr Laz akukonza chipani, DPP nayo ikukonza dziko, ndiye akabwera azizakamba chani cheni cheni. Magetsi pang’no pang’ono madandaulo akuchepa. Mwana anafunsa funso la magetsi uja is smiling. Economy zikuyenda, Miseu ponse ponse, fumbi likuchepa … and zomanga mangazitu ndi dziko lonse even ku mudzi kwao kwa a Dr Laz, nseu wa pamwamba ukupitako. Security, apolice magalimoto anapatsidwa etc.

Paja tinaletsa ndale zonyoza ndi za personal attacks, ndiye azizanena kuti chani? Za Kamuzu? What is he bringing to us?

99 Responses to "What Is Chakwera Bringing Us? Za Kamuzu?"

  1. Emmanuel Piffano   January 25, 2018 at 1:44 pm

    Magetsi,chakudya ndizina zotero sizinthu zomapangira MISONKHANO YOKOPERA ANTHU kuti adzavotere chipani chanucho.Ndiwufulu wanzika iliyonse kulandira chakudya,magetsi,maphunziro etc

    Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.