Queens’s Call Up Delights Mwai Kumwenda, As Mpinganjira Left Out 

20 Responses to "Queens’s Call Up Delights Mwai Kumwenda, As Mpinganjira Left Out "

 1. Amos Mika   November 5, 2017 at 2:24 pm

  akangochedwanso! abwelere basi

  Reply
 2. Joe West   November 5, 2017 at 5:58 pm

  These are the results when Talent mixesup with selfishness & this is all I know of a Malawian when we find a place in the civilized World. We always do the DON’TS just as one was news for a shameful reason, turning into a spitting Cobra.

  Reply
 3. Tony Madzukic Phiri   November 5, 2017 at 8:48 pm

  a Nam angoyambano business yophka mandasi bac ayamba kutichitisa manyaz

  Reply
 4. Mustafa Thomson   November 6, 2017 at 6:22 am

  Koma anayamba kudzimva masiku ano awa

  Reply
  • Lovemore Linyenje   November 6, 2017 at 8:02 am

   Man uyu ndi ster and not only ster shining only Malawi but the who world.
   Ndiye musanene kuti anaymba kudzimva ayi komanso anthu ena amapanga dala zinthu kuti wina alakwitse aziti amayerekedwa. Why Coach withdrew the Camp?
   Adadziwa kuti anthuwa ndindale.
   Ngati Mwawi analakwa bwanji sanapite pa air paja nkukamutsutsapo kuti ayi takusiya bkoz of this and that?????
   Mwawi Kumwenda z a Ster leave her Shine?

   Reply
  • Mustafa Thomson   November 6, 2017 at 8:26 am

   Man musawayikire kumbuyo awa

   Reply
 5. Davie Mdwazika   November 6, 2017 at 11:24 am

  Muziganiza musanachite zinthu umbuli basi

  Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.