Please Stop Embarrassing The Mighty DPP

One Response to "Please Stop Embarrassing The Mighty DPP"

  1. Samuel   August 1, 2018 at 7:37 pm

    You are right UTM ingaombe bwanji ifika nthawi yoti zipolopolo ziathela and that is the time to shoot back. Yatuta Chisiza and Dunduza Chisiza amounted an offensive attack using mass destruction machine gun in Mwanza. Asilikali athu adafa kwambiri chifukwa ankabweza moto osadziwa kuti adani abisala pati. Zidatengela Major Williams (Mzungu) kufufuza kuti zipolopolo zamdani zikuchokera pati. His advice to Malawi Army was simple do not shoot back. Dikilani zikaathera zipolopolo komanso akamva kuti kuliziii osamva kuomba kwa mfuti atuluka pamene abisalapo ndipo imeneyo ndiye nthawi yabwino yomuombera mdaniyo. Zidachitikadi ndipo asilikali athu adaombela Yatuta ndi Dunduza pamene adatuluka mudzenje. DPP upezeni mtima. Nkhono ya abale imawawa koma munthuyu wayamba kale kutopa. Khulupilirani CHILIMA SIMUMUMVA KUWAWA. Ng’oma yoliritsa sichedwa kusweka. Ugwireni mtima.

    Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.