On Rodney Jose, The folly of CSOs and Commentators

6 Responses to "On Rodney Jose, The folly of CSOs and Commentators"

 1. Anonymous   April 12, 2018 at 1:09 pm

  Tipangakeko kaye ka break pa nkhani zinazi.
  Nkhani ili mkamwamkamwa pano ndiya kukalamba kwa Pitala, Winiko wandiyimbira foni akuti akufuna Chilima azayimire DPP, nanga pa nkhani imeneyi mkutipo bwanji a Malawi Voice?
  Mmbuyo mwakhala mukubwebweta kwambiri za opperation landslide. Tiudzeni zoona!!!!

  Reply
 2. Anonymous   April 12, 2018 at 3:17 pm

  Eeeee tatiuzani manganizo anu a Malawi voice pankhani ya ukalamaba wa petulo mukuti bwanji?

  Reply
 3. Anonymous   April 12, 2018 at 4:46 pm

  Mwaziwa liti kuti wakalamba?

  Reply
 4. Anonymous   April 13, 2018 at 7:18 am

  If truth be told

  Reply
 5. Anonymous   April 13, 2018 at 3:18 pm

  Mukusiya kukamba za agogo anu amatupi plastic zoika mphepete mwamoto, mkumalimba ndi munthu wamphamvu ndi wa school yake. Kwinaku certificate ya PSLC mulibenso, business mulibe, ka itel adachita kukupatsani. Kumangokamba zoduka mutu nthawi ndi nthawi. Olo ambuyako kuwapatsa u village head kulephera. Kungobadwa otemberereka banja lonse zoona. Nde mkumalubwalubwa ndi ukalamba wa Peter. Ena mukulemba za ukalamba wa peter ndinu mbava munazolowera kuba nthawi ya udf ndi pp. Mukusiya mavuto anu mkumalimbana ndi munthu. Komabe olo mudzibwaruka palibe chomwe mupindule. Amisala anzanu ati ndi ma mp achina kalindo ndi ngalande ndi ndani. Za zii. Posachedwa apititsidwa ku mental mumfunse wamisala waku thyolo uja.

  Reply

Leave a Reply to Anonymous Cancel reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.