Mkulu Wa Chipani Cha UTM Atukwana A Bakili Muluzi Zamusalu

Mmodzi mwa atsogoleri a chipani cha United Transformation Party (UTM) a Limbikani Henry Mhango atukwana mtsogoleri wopuma wa dziko lino a Bakili Muluzi ati chifukwa chozudzula zomwe atsogoleri ena achipanicho akuchita ponyoza pulesident wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika. Izi ndi zomwe a Mhango adalemba pa tsamba lawo la FACEBOOK:

 

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.