‘Foolish Galatians’ Back In Parliament

Malawi Congress Party (MCP) Members of Parliament today returned to the August House.

MCP Parliamentarians, led by Leader of Opposition, Lazarus Chakwera, on Monday afternoon walked out of the august House protesting government’s delay to table the Electoral Reforms Bills.

58 Responses to "‘Foolish Galatians’ Back In Parliament"

 1. Francis Zipondo   December 6, 2017 at 12:31 pm

  DPP inawina masankho ili kunja kwa boma en now they’re inside,just wait & see.Chakwela 2019 abweleraso ku ubusa,iswear!!

  Reply
 2. Francis Zipondo   December 6, 2017 at 12:37 pm

  Chakwela amaona ngati akanyanyala zokambilana parliament isiya zokambirana nkumadikila iyeyo kkkkk AGALATIYA OPEPELA

  Reply
 3. James S Phiri   December 6, 2017 at 5:16 pm

  Amcp, mukanakhala anzeru bwezi mukumauza mtundu wamalawi kuti ma company onse anagulisidwa aboma abwelere kuti anthu apeze ntchito, economy inhale yokhazikika, piano mukuli mbikila zaxii zoti sizing painful ire amalawi olo pang,ono, pangani zomanga dziko kuti zithu zitsike wakumudzi Wa mtauni sangadye zimenezo,buyomu UDF imkaudza anthu kuti akagulisa macompany aboma amalawi adzapindula Ndalama ifzakhazikika , lero skuvutika ndi ndani, bwinotu bwino

  Reply
 4. Shokoloko Bangosha   December 6, 2017 at 5:57 pm

  This country is too small to practice politics of hate. Even propaganda has to be civilized.

  Reply
 5. Calisto Mahonya   December 6, 2017 at 6:42 pm

  A PAC akwera chakwera,komatu musaiwale kuti mulungu amalanga anthu osamumvera.anasiya ubusa nkuyamba ndale.apac wanso akuti dabwitsa bwanji sanabweletse billyi nthawi ya JOYCE BANDA.inunso mukangolembetsa chipan chanu .MUKUNYOZETSA MPINGO WA YESU Woyerawu.

  Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.