Drama In Parliament As Cracks In MCP Deepen

53 Responses to "Drama In Parliament As Cracks In MCP Deepen"

 1. Anonymous   February 25, 2018 at 1:53 am

  Ndimadzifunsa mafunsoawa nthawi zonse ndikangomva mau akuti Dpp bomaaaa!!! Dpp 2019 bomaaaa!!!

  Kodi Mkulu wa zachisankho malemu Markson Mbendera amkalira chiyani polengeza zotsatira za chisankho cha President cha mchaka cha 2014?
  Kodi adafa chifukwa chiyani?

  Kodi Issah Njaudyu adamupha ndani?
  Nanga adaphedwa chifuwa chiyani?

  Mafunso awa amandisowa mayankho chonde mwina wina akudziwa aliuze dziko la Malawi.

  Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.