Burundian Arrested For Defiling, Impregnating Malawian Girl

30 Responses to "Burundian Arrested For Defiling, Impregnating Malawian Girl"

 1. Arnold Michael Mlima   November 8, 2017 at 7:51 pm

  Simwana Ameneyo Zachamba Eti Ine Ndikuphaka Ka Super 16 Kakaphulika Mudziti Ndakagwiririla?

  Reply
 2. Mandala Cool Musayiwale Kondowe   November 8, 2017 at 8:08 pm

  mmmmm defiling ? nut to impregnating? ok bobo

  Reply
 3. Joel Gebu   November 8, 2017 at 8:23 pm

  Timva ziti ena akut mkulu wamangidwayu anali mphizitsi now inu mukut ndi Mbulundi!/

  Chichitikireni chisankho chapadera chija mukungolemba zobalalika zokhazokhatu

  Malawi 24 ikut mkuluyi ndi mphuzitsi

  Reply
 4. Calvin Mandime   November 8, 2017 at 8:50 pm

  Amasulidwe munthuyi ngosalakwa kodi simufuna ana akunja?

  Reply
 5. Kenneth Chayenda   November 8, 2017 at 11:06 pm

  osaonesa zomwe mwapha dzulo mulimbe kupha munthu mulimbe ngati galu anthu inu mukuonesa za ziiii osaonesa ubongo wadzulo ndi magazi ochita kusamba aja amalawi

  Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.