Blue-Sea At Nchalo As APM Outlines Development Programmes Of Transformation

13 Responses to "Blue-Sea At Nchalo As APM Outlines Development Programmes Of Transformation"

 1. Machitidwe Sepitala   February 5, 2018 at 6:25 am

  Za ntiiiiiii, chimanga munagula kwa alimi kapena mavenda?????

  Reply
 2. Divala Khomba George Faiti   February 5, 2018 at 7:16 am

  Ma plan anu alephereka mumaganiza ngati chaka chinoso tikolola ngati last year cholinga chimanga cha last year mupangire campaign ndiye Mulungu wakutsutsani chakudya chimenecho palibe kulandira campaign

  Reply
  • Joe West   February 5, 2018 at 10:13 am

   Mulungu wakwiya kwambiri ndi Azibusa amene akusiya ntchito zake nkumakatumikira za Dziko. A Chakwera anasiya kulandira cha Khumi kuti ayambe kulipilitsa ndi kulandira Ndalama za Misonkho.

   Reply
 3. Innocent Nyangulu   February 5, 2018 at 8:04 am

  Kodi chimangachi mzagawa ulere?

  Reply
 4. Kwesi Chigwe Chef   February 5, 2018 at 8:40 am

  Chongokwanila kudya anthu akumulanje basi.ku zomba mutitani

  Reply
 5. Mapemba Michael   February 5, 2018 at 9:12 am

  Much ado about nothing! That was a slip of a tongue. I am sure it should be 234000 metric tonnes.

  Reply

Leave a Reply

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.