DPP Yokha Sidzalowanso M’boma: Anamatetule Amenewa Adachezera Kututa Ndalama Ku Sanjika Mpakana Kuthyola Chitseko Atamwalira Bingu-Watero Joyce Banda

JB NDI BINGUMtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda wati ndi zokhumudwitsa kwambiri kuti atsogoleri a chipani cha DPP adachezera kututa ndi kuthawitsa ndalama ku nyumba ya chifumu ya Sanjika mpakana kuthyola chitseko nthawi ya maliro a Bingu wa Mutharika.

“Anamatetule amenewa ndi oipa, adathyola chitseko pothawitsa ndalama ndipo mpakana lero chitsekocho sindidachikonzetse kuti udzakhale umboni. Koma ine ndikulumbira kuti ndalama zanga sindizabitsa koma kugwiritsa ntchito moyenera basi. Ndipo lonjezo langa ndi lakuti ineyo sindizakukhumudwitsani.

“Ndipo kaya wina afune kaya asafune, chipani cha DPP chokha sichidzalowanso m’boma,” watero Banda.

Mai banda amayankhula izi ku Chintheche, m’boma la Nkhatabay tsiku Loweluka.

31 Comments for “DPP Yokha Sidzalowanso M’boma: Anamatetule Amenewa Adachezera Kututa Ndalama Ku Sanjika Mpakana Kuthyola Chitseko Atamwalira Bingu-Watero Joyce Banda”

 1. priscilla

  dpp wil win joYCE whethr u lyk it or nt we are tired with damn tingz

 2. nalisero

  Sabola wakale sawawa….mukunenayo is history……koma ife timavota on today’s experience and feelings…….DPP idzalamulanso posachedwapa

 3. Dokotiwo s. Am’midzi zoona alibe internet but they have relatives in town who have. The suffering they are going through because of Joyce’s policies is unimaginable. The party with real grassroot support is DPP followed by UDF. Am just telling you in advance to save you from blood pressure in 2014.

 4. ok?if dpp is not coming bck!joyce bandayo afune asafune peter yekha 2014 boma whether with dpp or not!

 5. Ngozi

  Joice, you loose mouth will make you fail.Who can vote for mbuli ngati Joice ndi Kachali muli busy kuba chuma cha boma ndikumalalata.Tikudziwa mukuopa DPP. DPP tidzaiike mboma ndi ife basi osati Joice, mbuli yotheratu. Ukhalira yomweyo yokuba ndi ndi kulalataa malawi sadya ndale, wamva???

 6. Patriot

  Amachita kuthyola manda nkumatulutsa makobiri ankhani nkhani.
  Mbava izi.
  SADZALAMULIRANSO DZIKO LINO AWA.

Leave a Reply

Log in | Designed By Malawi Voice